Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+