2 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+ 2 Mbiri 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wake, mʼmwezi woyamba, iye anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova komanso anazikonza.+
29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+
3 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wake, mʼmwezi woyamba, iye anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova komanso anazikonza.+