-
1 Samueli 26:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wanu mʼmanja mwanu.+ Bwanji ndimubaye ndi mkondo nʼkumukhomerera pansi? Ndimubaya kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.” 9 Koma Davide anauza Abisai kuti: “Ayi, usamubaye. Ndani angavulaze wodzozedwa wa Yehova+ nʼkukhala wopanda mlandu?”+
-