Salimo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyamukani, inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga! Mudzamenya adani anga onse pachibwano.Mudzaphwanya mano a anthu oipa.+
7 Nyamukani, inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga! Mudzamenya adani anga onse pachibwano.Mudzaphwanya mano a anthu oipa.+