-
Deuteronomo 17:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la Chilamulo ichi, kuchokera mʼbuku limene* Alevi omwe ndi ansembe amasunga.+
19 Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a Chilamulo ichi, komanso kutsatira malangizo ake.+
-