1 Mafumu 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Atipatse mtima wofuna kuyenda mʼnjira zake zonse+ komanso kutsatira malamulo ake, malangizo ake ndi ziweruzo zake zimene analamula makolo athu.
58 Atipatse mtima wofuna kuyenda mʼnjira zake zonse+ komanso kutsatira malamulo ake, malangizo ake ndi ziweruzo zake zimene analamula makolo athu.