Salimo 86:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndisonyezeni chizindikiro cha* ubwino wanu,Kuti anthu amene amadana nane aone ndipo achititsidwe manyazi, Chifukwa inu Yehova ndi amene mumandithandiza komanso kundilimbikitsa. Salimo 102:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandibisire nkhope yanu pamene ndili pamavuto aakulu.+ Tcherani khutu lanu kwa ine.*Ndiyankheni mofulumira pamene ndikuitana.+
17 Ndisonyezeni chizindikiro cha* ubwino wanu,Kuti anthu amene amadana nane aone ndipo achititsidwe manyazi, Chifukwa inu Yehova ndi amene mumandithandiza komanso kundilimbikitsa.
2 Musandibisire nkhope yanu pamene ndili pamavuto aakulu.+ Tcherani khutu lanu kwa ine.*Ndiyankheni mofulumira pamene ndikuitana.+