Salimo 89:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa ndanena kuti: “Chikondi chanu chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwanu kudzakhala kumwamba mpaka kalekale.” Salimo 119:152 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 152 Kale kwambiri, ndinaphunzira zokhudza zikumbutso zanu,Kuti munazikhazikitsa kuti zikhalepo mpaka kalekale.+
2 Chifukwa ndanena kuti: “Chikondi chanu chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwanu kudzakhala kumwamba mpaka kalekale.”
152 Kale kwambiri, ndinaphunzira zokhudza zikumbutso zanu,Kuti munazikhazikitsa kuti zikhalepo mpaka kalekale.+