Deuteronomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu woona, Mulungu wokhulupirika, amene amasunga pangano lake ndiponso amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amamukonda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo 1,000.+
9 Inu mukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu woona, Mulungu wokhulupirika, amene amasunga pangano lake ndiponso amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amamukonda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo 1,000.+