Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye wakhazikitsa dziko lapansi pamaziko ake.+Silidzasunthidwa pamalo ake* mpaka kalekale.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼbadwo umapita ndipo mʼbadwo wina umabwera,Koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.+