Salimo 86:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tetezani moyo wanga chifukwa ndine wokhulupirika.+ Pulumutsani mtumiki wanu amene amakukhulupirirani,Chifukwa ndinu Mulungu wanga.+ Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’
2 Tetezani moyo wanga chifukwa ndine wokhulupirika.+ Pulumutsani mtumiki wanu amene amakukhulupirirani,Chifukwa ndinu Mulungu wanga.+
10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’