Salimo 119:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzaganizira mozama* malamulo anu,+Ndipo ndidzayangʼanitsitsa njira zanu.+