2 Samueli 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzakhalabe wosalakwa+ pamaso pake,Ndipo ndidzayesetsa kupewa cholakwa.+ Miyambo 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu wanzeru amachita zinthu mosamala ndipo amapewa zoipa,Koma wopusa amachita zinthu mosasamala* ndipo amakhala wodzidalira.
16 Munthu wanzeru amachita zinthu mosamala ndipo amapewa zoipa,Koma wopusa amachita zinthu mosasamala* ndipo amakhala wodzidalira.