Chivumbulutso 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye ndinamva mngelo amene ali ndi ulamuliro pa madzi akunena kuti: “Inu Mulungu amene mulipo ndi amene munalipo,+ inu Wokhulupirika,+ ndinu wolungama chifukwa mwapereka ziweruzo zimenezi,+ Chivumbulutso 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova* Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ ziweruzo* zanu ndi zoona komanso zolungama.”+
5 Ndiye ndinamva mngelo amene ali ndi ulamuliro pa madzi akunena kuti: “Inu Mulungu amene mulipo ndi amene munalipo,+ inu Wokhulupirika,+ ndinu wolungama chifukwa mwapereka ziweruzo zimenezi,+
7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova* Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ ziweruzo* zanu ndi zoona komanso zolungama.”+