Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyera.+Ali ngati siliva woyengedwa mungʼanjo yadothi nthawi zokwanira 7. Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale.
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo zigamulo zanu zonse zolungama zidzakhalapo mpaka kalekale.