Salimo 119:97 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!+ Ndimaganizira mozama* chilamulocho tsiku lonse.+