2 Samueli 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova andipatse mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso chifukwa choti ndine wosalakwa pamaso pake.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+
25 Yehova andipatse mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso chifukwa choti ndine wosalakwa pamaso pake.+
21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+