Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 101:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mʼnyumba yanga simudzakhala munthu wachinyengo,

      Ndipo wabodza aliyense sadzaima pamaso panga.

  • Salimo 119:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndithandizeni kuti ndisakhale munthu wachinyengo,+

      Ndipo mundikomere mtima pondipatsa chilamulo chanu.

  • Salimo 119:104
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 104 Ndimachita zinthu mozindikira chifukwa cha malamulo anu.+

      Nʼchifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena