Salimo 139:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumandiona* ndikamayenda komanso ndikagona.Mumadziwa chilichonse chimene ndikuchita.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+ Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati Yehova amaona bwinobwino amene ali mʼManda* ndiponso malo achiwonongeko,*+ Ndiye kuli bwanji zimene zili mʼmitima ya anthu?+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+
21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+
11 Ngati Yehova amaona bwinobwino amene ali mʼManda* ndiponso malo achiwonongeko,*+ Ndiye kuli bwanji zimene zili mʼmitima ya anthu?+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+