Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndimalengeza uthenga wabwino wa chilungamo mumpingo waukulu.+ Onani! Sinditseka pakamwa panga,+Monga mmene mukudziwira, Inu Yehova.
9 Ndimalengeza uthenga wabwino wa chilungamo mumpingo waukulu.+ Onani! Sinditseka pakamwa panga,+Monga mmene mukudziwira, Inu Yehova.