Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Osangalala ndi anthu oyera mtima+ chifukwa adzaona Mulungu.