Salimo 91:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Palibe tsoka limene lidzakugwere,+Ndipo palibe mliri umene udzayandikire tenti yako. Miyambo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+Koma anthu oipa ndi amene adzakumane ndi mavuto ambiri.+
21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+Koma anthu oipa ndi amene adzakumane ndi mavuto ambiri.+