Salimo 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munalola kuti munthu wamba atipondeponde.*Tinadutsa pamoto ndi pamadzi,Kenako munatibweretsa pamalo ampumulo. Yesaya 51:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzaika kapu imeneyi mʼmanja mwa amene akukuvutitsa,+Amene amakuuza kuti, ‘Werama kuti tiyende pamsana pako.’ Choncho unachititsa kuti msana wako ukhale ngati malo oti azipondapo,Ngati msewu woti azidutsamo.”
12 Munalola kuti munthu wamba atipondeponde.*Tinadutsa pamoto ndi pamadzi,Kenako munatibweretsa pamalo ampumulo.
23 Ndidzaika kapu imeneyi mʼmanja mwa amene akukuvutitsa,+Amene amakuuza kuti, ‘Werama kuti tiyende pamsana pako.’ Choncho unachititsa kuti msana wako ukhale ngati malo oti azipondapo,Ngati msewu woti azidutsamo.”