Ezara 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli ndinu wolungama+ chifukwa ife tidakali ndi moyo mpaka lero. Taima pamaso panu mʼmachimo athu, ngakhale kuti nʼzosatheka kuima pamaso panu chifukwa cha zimenezi.”+ Nehemiya 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+
15 Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli ndinu wolungama+ chifukwa ife tidakali ndi moyo mpaka lero. Taima pamaso panu mʼmachimo athu, ngakhale kuti nʼzosatheka kuima pamaso panu chifukwa cha zimenezi.”+
33 Inu mwachita zinthu molungama pa zonse zimene zatichitikira. Mwachita zinthu mokhulupirika koma ife ndi amene tachita zinthu zoipa.+