4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.
7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide chifukwa cha pangano limene anachita ndi Davide,+ poti anamulonjeza kuti adzamʼpatsa nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+