Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+
2 Pemphero langa likhale ngati zofukiza+ zokonzedwa pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+