Miyambo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usadzudzule wonyoza chifukwa angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+ Miyambo 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Menya munthu wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere,+Ndipo dzudzula munthu womvetsa zinthu kuti awonjezere zimene akudziwa.+ Miyambo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera+Amakhala ngati ndolo yagolide ndiponso ngati chokongoletsera chagolide woyenga bwino.
25 Menya munthu wonyoza+ kuti wosadziwa zinthu achenjere,+Ndipo dzudzula munthu womvetsa zinthu kuti awonjezere zimene akudziwa.+
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera+Amakhala ngati ndolo yagolide ndiponso ngati chokongoletsera chagolide woyenga bwino.