2 Mbiri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+ Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayangʼana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+
12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+
15 Maso anga amayangʼana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+