1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amuphe.+ Apa tsopano Yonatani anadziwa kuti bambo ake atsimikiza zopha Davide.+ 1 Samueli 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Sauli anafika mbali ina ya phiri limene Davide ndi amuna amene anali naye anabisala. Zitatero Davide anayamba kukonzeka mwamsanga kuti athawe+ Sauli. Pa nthawiyi nʼkuti Sauli ndi asilikali ake atatsala pangʼono kupeza Davide ndi amuna amene anali naye.+ 1 Samueli 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amuphe.+ Apa tsopano Yonatani anadziwa kuti bambo ake atsimikiza zopha Davide.+
26 Kenako Sauli anafika mbali ina ya phiri limene Davide ndi amuna amene anali naye anabisala. Zitatero Davide anayamba kukonzeka mwamsanga kuti athawe+ Sauli. Pa nthawiyi nʼkuti Sauli ndi asilikali ake atatsala pangʼono kupeza Davide ndi amuna amene anali naye.+
29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*