2 Samueli 22:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo+ ndiponso Wondipulumutsa.+ 3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.
2 Iye anati: “Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo+ ndiponso Wondipulumutsa.+ 3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.