9 Mukabwerera kwa Yehova, abale anu ndi ana anu adzachitiridwa chifundo ndi anthu amene anawagwira+ ndipo adzawalola kubwerera mʼdzikoli.+ Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi wachisomo komanso wachifundo+ ndipo sadzayangʼana kumbali mukabwerera kwa iye.”+