Luka 10:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso mukalowa mumzinda ndipo iwo nʼkukulandirani, muzidya zimene akukonzerani, 9 muzichiritsanso odwala amene ali mmenemo komanso muziwauza kuti: ‘Ufumu wa Mulungu wakuyandikirani.’+
8 Komanso mukalowa mumzinda ndipo iwo nʼkukulandirani, muzidya zimene akukonzerani, 9 muzichiritsanso odwala amene ali mmenemo komanso muziwauza kuti: ‘Ufumu wa Mulungu wakuyandikirani.’+