Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:50, 51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Nʼchifukwa chake ndidzakuyamikani inu Yehova pakati pa mitundu ya anthu.+

      Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+

      51 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake;+

      Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,

      Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”+

  • 1 Mbiri 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Muimbireni, muimbireni nyimbo* zomutamanda,+

      Ganizirani mozama* ntchito zake zonse zodabwitsa.+

  • Aroma 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komanso kuti anthu a mitundu ina alemekeze Mulungu chifukwa cha chifundo chake,+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena