Salimo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+