Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu kuti:

      “Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zimakhala mmenemo.+

  • Chivumbulutso 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena