Yesaya 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsiku limenelo, anthu amene ali ndi vuto losamva adzamva mawu amʼbuku,Ndipo maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzamasuka kumdima wandiweyani ndipo adzayamba kuona.+ Yesaya 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzatsegulidwa,+Ndipo makutu a anthu amene ali ndi vuto losamva adzayamba kumva.+
18 Tsiku limenelo, anthu amene ali ndi vuto losamva adzamva mawu amʼbuku,Ndipo maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzamasuka kumdima wandiweyani ndipo adzayamba kuona.+
5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzatsegulidwa,+Ndipo makutu a anthu amene ali ndi vuto losamva adzayamba kumva.+