Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu amene mumasonyeza anthu masauzande ambiri chikondi chokhulupirika koma mumabwezera kwa ana,* zolakwa za abambo awo.+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu ndi wamphamvu ndipo dzina lanu ndinu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Yuda 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhalenso Inoki,+ wa mʼbadwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova* anabwera ndi angelo ake masauzandemasauzande+
18 Inu amene mumasonyeza anthu masauzande ambiri chikondi chokhulupirika koma mumabwezera kwa ana,* zolakwa za abambo awo.+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu ndi wamphamvu ndipo dzina lanu ndinu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
14 Ngakhalenso Inoki,+ wa mʼbadwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova* anabwera ndi angelo ake masauzandemasauzande+