1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+ 1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse.
27 Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba imene ndamangayi?+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse.