Oweruza 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa+ ndipo akufika anangoona mwana wake wamkazi akubwera kudzamʼchingamira, akuimba maseche komanso akuvina. Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.
34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa+ ndipo akufika anangoona mwana wake wamkazi akubwera kudzamʼchingamira, akuimba maseche komanso akuvina. Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.