Deuteronomo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+ Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu komanso woyenera kutamandidwa kwambiri,+Palibe amene angamvetse ukulu wake.+
24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+