Salimo 119:127 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Nʼchifukwa chake ine ndimakonda malamulo anuKuposa golide, ngakhale golide wabwino kwambiri.*+ Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva,Komanso kudziwa zinthu mʼmalo mwa golide woyenga bwino kwambiri,+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva,Komanso kudziwa zinthu mʼmalo mwa golide woyenga bwino kwambiri,+