1 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mumtima mwanga sindikudzitsutsa pa nkhani iliyonse. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, chifukwa Yehova* ndi amene amandifufuza.+
4 Mumtima mwanga sindikudzitsutsa pa nkhani iliyonse. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, chifukwa Yehova* ndi amene amandifufuza.+