Salimo 119:133 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Nditsogolereni ndi mawu anu kuti ndiyende mʼnjira yotetezeka.Musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+
133 Nditsogolereni ndi mawu anu kuti ndiyende mʼnjira yotetezeka.Musalole kuti choipa chilichonse chindilamulire.+