Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,

      Ndipo zimene ndikuganizira mozama mumtima mwanga+ zidzasonyeza kuti ndine wozindikira.

  • Salimo 51:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,

      Kuti pakamwa panga patamande inu.+

  • Salimo 143:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndikukumbukira masiku akale.

      Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+

      Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.

  • Afilipi 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chomalizira abale, pitirizani kuganizira* zinthu zilizonse zoona, zilizonse zofunika kwambiri, zilizonse zolungama, zilizonse zoyera, zilizonse zolimbikitsa chikondi, zilizonse zimene anthu amaziyamikira, khalidwe labwino lililonse komanso chilichonse chotamandika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena