Salimo 71:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndakhala ndikudalira inu kuchokera tsiku limene ndinabadwa.Inu ndi amene munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga.+ Ndimakutamandani nthawi zonse. Salimo 139:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maso anu anandiona ngakhale pamene ndinali mluza.*Ziwalo zanga zonse zinalembedwa mʼbuku lanuMʼbukumo munalembedwa za masiku amene zinapangidwa,Zinalembedwa chiwalo chilichonse chisanapangidwe.
6 Ndakhala ndikudalira inu kuchokera tsiku limene ndinabadwa.Inu ndi amene munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga.+ Ndimakutamandani nthawi zonse.
16 Maso anu anandiona ngakhale pamene ndinali mluza.*Ziwalo zanga zonse zinalembedwa mʼbuku lanuMʼbukumo munalembedwa za masiku amene zinapangidwa,Zinalembedwa chiwalo chilichonse chisanapangidwe.