Mateyu 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva chisoni* chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+ Maliko 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane+ ndipo anayamba kumva chisoni komanso kuvutika kwambiri mumtima mwake.
38 Kenako anawauza kuti: “Ine ndikumva chisoni* chofa nacho. Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+
33 Popita kumeneko anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane+ ndipo anayamba kumva chisoni komanso kuvutika kwambiri mumtima mwake.