Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nʼchifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali? Nʼchifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya mavuto?+