Yohane 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu amene munawatenga mʼdziko nʼkundipatsa, ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine ndipo iwo amvera mawu anu.
6 Anthu amene munawatenga mʼdziko nʼkundipatsa, ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine ndipo iwo amvera mawu anu.