Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima.