Salimo 118:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditsegulireni mageti achilungamo.+Ndidzalowa mmenemo ndipo ndidzatamanda Ya. Salimo 122:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo tsopano mapazi athu aimaPamageti ako iwe Yerusalemu.+